Amayi alimbikitsa mtendere munyengo ya chisankho m’boma la Nkhotakota
Gulu la amayi lolimbikitsa bata ndi mtendere la Kanyenda Women’s Forum m'boma la Nkhotakota lati lipitiriza kugwiritsa ntchito njira zosiyanasiyana pofalitsa uthenga wake pamene dziko lino layandikira tsiku la chisankho. Wapampando wa gululi, Alinafe Major Kamunthu ndiye wanena izi pamapeto a...